Best Zambia Online juga

Kufunafuna mndandanda wa bwino Zambia Intaneti juga? Yang'anani patsogolo - onani tsamba athu ndi kupeza zabwino zonse Zambia juga Intaneti!
Show more Hide

Mobile friendly

Players are welcome

None

Filter

Sort by:

None

Sort by:

Promoted
Latest
Best Casinos
Bonus Rating
Trust Rating
Game Rating
Usability Rating

2.8

 • 2.5
 • 3.9
 • 2.1
 • 2.6
Welcome 100% and 100 Spins in Starsburst!
 • Launched 01.Dec.2019
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, Pragmatic Play, Betsoft
 • Licenсes Curaçao

WR40x,

Min Dep €20

2.8

 • 2.5
 • 3.2
 • 2
 • 3.5
100% up to €500 + 100 Free Spins
 • Launched 09.Mar.2020
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, Pragmatic Play, Betsoft
 • Licenсes Curaçao

WR30x,

Min Dep €20

2.6

 • 4.5
 • 1.6
 • 2.5
 • 1.8
200% Welcome Bonus + 25 Free Spins
 • Launched 08.Jun.2016
 • Software Rival
 • Licenсes Curaçao

WR40x,

Min Dep $25,

CodeLOVELY200

3

 • 2.5
 • 3.7
 • 2.1
 • 3.8
100% Bonus up to €500 + 200 Free Spins
 • Launched 2019
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, NextGen, Pragmatic Play
 • Licenсes Curaçao

WR30x,

Min Dep €20

3.1

 • 2.5
 • 4
 • 2.2
 • 3.8
100% Bonus up to €500 and 200 Free Spins
 • Launched 2019
 • Software NetEnt, Microgaming, Evolution, Pragmatic Play, Betsoft
 • Licenсes Curaçao

WR30x,

Min Dep €20

2.6

 • 2.5
 • 2.9
 • 2.2
 • 2.8
300% Up To €1000 + 100 Free Spins
 • Launched 2019
 • Software NetEnt, Evolution, NextGen, Pragmatic Play, Betsoft
 • Licenсes Curaçao

WR20x,

Min Dep €20

Kodi mukudziwa kuti mukhoza kupeza phindu lalikulu pamene mukusewera ku kasino ya pa intaneti yomwe ndi yovomerezeka ndi malamulo a dziko lino? Mwacitsanzo, mzinda wa Lusaka uli ndi malo ambiri amene anthu angapezeko makasino ngakhalenso a pa intaneti. Kuwonjezera pamenepa, mumzindawu muli makina ambirimbiri komanso makompyuta osewerera magemu osiyanasiyana othandiza anthu kupeza phindu lalikulu. Malamulo a dziko lina amavomereza kuti anthu a zaka zosacepera pa 18 akhoza kusewera pa jakipoti ndi kupeza ndalama zambiri.

Makasino a pa Intaneti ku Zambia

Malo oterewa pa intaneti akuyenera kukhala ndi magemu ambiri ndithu kuti munthu athe kusankha gemu yomwe angakonde. Ena mwa magemuwo ndi monga otsatirawa:

Kugwiritsa nchito makadi a pa kompyuta. Munthu angathe kugwiritsira nchito foni kapena kompyuta posewera gemu imeneyi. Pali mitundu yambirimbiri ya gemu ya makadi yomwenso imaseweredwa mu njira zosiyanasiyana. Gemu ina munthu angasewere payekha, koma ina anthu angapo amayenera kusewera limodzi mochita kugawana m’magulu. Nthawi zinanso anthu angapo angasewere mocita kugawana mu magulu awiri ndi kumasewera mopikisana. Gulu lomwe lingapambane ndi limenenso limatenga ndalama zomwe anabecherana. Pa masewera amenewa, omwe tinganene kuti ndi kasino ya pa intaneti, anthu amatha kucita mwayi ndi kupeza ndalama zoculuka zedi.

Masewera a pa kompyuta ogwiritsira nchito manambala. Gemu imeneyi ingaseweredwenso ndi munthu mmodzi kapena angapo pa nthawi imodzi. Kuti munthu asewere gemu imeneyi, yomwe ili ngati jakipoti koma ya pa foni kapena pa kompyuta, munthu amafunika kuika ndalama pa nambala imene wasankha, pa manambala amene ali pa bodi yozungulira yokhala ndi manambala ambirimbiri. Ndiyeno pamafunika kupukusa bodiyo kuti azungulire mwa mphamvu. Bodiyo ikaima ndipo nambala ikaima pa mzere wolondola, ndiye kuti munthu amene amasewerayo wawina ndalama zoculuka kwambiri mogwirizana ndi pamalo amene anabechera. Angati amene akusewera ndi anthu angapo pa nthawi imodzi, ndiye kuti amangofunika kuika ndalama zawo pa manambala angapo osiyanasiyana. Zimathekanso kusewera gemuyi, imene ndi yofanana ndi jakipoti, pogawana mu magulu awiri.

Masewera ogwiritsira nchito madaisi. Pa masewera amenewa, munthu mumodzi angasewere payekha kapena anthu angapo angasewere nthawi imodzi. Zimakhalanso zotheka kuti anthu angapo apange magulu awiri ndi kusewera gemuyi, imene tinganene kuti ndi kasino ya pa intaneti, mocita kupikisana. Gemu imeneyi ingathe kuseweredwa pogwiritsira nchito foni kapena kompyuta. Cofunika ndi cakuti pakhale intaneti basi.

Kodi Malamulo a Dziko la Zambia Amavomereza?

Malo aliwonse ovomerezeka amene anthu akucita masewera okhudza ndalama, monga jakipoti, amayenera kulembetsedwa ku boma mogwirizana ndi malamulo a dziko la Zambia. Ngakhalenso malo amene amapezeka pa intaneti pomwe munthu angathe kusewera pa nthawi iliyonse komanso pa malo ena aliwonse amayeneranso kukhala ogwirizana ndi malamulo a dziko lino. Ndipo dzikoli limapereka ziphaso zitatu zosiyanasiyana kwa munthu yemwe akufuna kutsegula kasino. Zilinso cimodzimodzi ngakhale ngati akufuna kutsegula malo oterewa pa intaneti pokha. Ubwino wocita zimenezi ndi wakuti anthu omwe asankha kusangalala ndi magemu osiyanasiyana kumalo otere amakhala otetezeka ndiponso ndalama zawo zimakhala zotetezekanso cifukwa sagaberedwe mwacinyengo. Kuwonjezera pamenepa, ngati patacitika ngozi yadzidzidzi yomwe yakhudza anthu omwe ali mu kasino yotereyi, ovulalawo amayenera kulandira cipepeso kucokera kwa eni a malowo, mogwirizana ndi malamulo a dziko lino la Zambia. Zili cimodzimodzinso ndi malo otere omwe amapezeka pa intaneti pokha. Ngati zinthu zina zokhudza netiweki zitasokonezeka zimene zingacititse kuti anthu amene akusewera magemu osiyanasiyana aluze ndalama, ena ake a malolowo amayenera kupereka ndalama ya cipukuta misozi kwa anthu okhudzidwawo. Cinthu cinanso cofunika kwambiri ndi cakuti anthu amene apambana pa masewera aliwonse pa kasino ya pa kompyuta amayenera kulandira ndalama zawo nthawi yomweyo popanda kuzengereza. Izi zimacitika cifukwa ndalama zomwe apambanazo zimayenera kulowa ku akaunti yawo ya ku banki kapena akaunti yawo ya pa foni. Motero malamulo onse a boma akatsatiridwa, zimathandiza kuti mbali zonse zokhudzidwa zikhale zotetezeka.

Mawu Omaliza

Malinga ndi zimene taonazi, n’zotheka ndithu munthu kukhala mponda matiki ku Zambia komwekuno popanda kupita kukagwira nchito m’mayiko akunja. Ndipo zimenezi zingatheke popanda kukhetsa thukuta ngakhale pang’ono! Ndipo masiku ano mungathe kusewera magemu onse a ku kasino pa foni yanu kapena pa kompyuta yanu.